*Verse 1*
Mbuye ndi thanthwe lolimba, Ndipousira chimphepo,
M’zovuta takhazikika, ndi pousira chimphepo.
Ndiye mnthuzi pausana, Ndipousira chimphepo M’usiku saopsa mantha, Ndipousira chimphepo.
*Chorus*
Yesu ndi thanthwe m’dziko lotopesa, lotopetsa, lotopetsa
Yesu ndi thanthwe m’dziko lotopetsa
Ndi pousira chimphepo.
*Verse 2*
Namondwe akatizinga, Ndipousira chimphepo. Panopa sitisunthidwa, Ndipousira chimphepo,
Thanthwe langa looosira, Ndipousira chimphepo. Ndinu wotithangatira, Ndipousira chimphepo.
Chorus
Yesu ndi thanthwe m’dziko lotopesa, lotopetsa, lotopetsa
Yesu ndi thanthwe m’dziko lotopetsa
Ndi pousira chimphepo.