Chorus
Kulibe Onga inu Yesu
Kulibe Onga inu Mesiya
Kulibe Onga inu Yawe
Kulibe wina angafane nanu
Yawe ndinu nokha.
Verse 1
Ambuye inu mwayeneladi
Ulemu onse eeeh eeeh
Ndi matamando
Kunthawi za nthawi zonse Eeeeh eeeh
Popeza ndinu Alpha and Omega chiyambi ndimathelooo
Olungama osakwiya nsanga ndinu Yehova
Chorus
Kulibe Onga inu Yesu
Kulibe Onga inu Mesiya
Kulibe Onga inu Yawe
Kulibe wina angafane nanu
Yawe ndinu nokha.
Verse 2
Ndayenda Yenda
Padziko lonse
Sinampeze Onga inu
Ndazungulira konse konse sim’nampeze
Ofana nanu
Mwini Moyo siliva ndi golide zonse ndi zanuu Yaweee
Olungama osakwiya nsanga ndinu Yehova.
Chorus
Kulibe Onga inu Yesu
Kulibe Onga inu Mesiya
Kulibe Onga inu Yawe
Kulibe wina angafane nanu
Yawe ndinu nokha.