Chorus
Ndaimba foni kumwamba Ambuye wandiyakha zokhumba mtima wanga zosowa pamoyo wanga Ambuye wandiyakha
Verse 1
Ndinali ndani ine pamaso pa anthuwa amzanga kundiseka abale kundisala abwenzi kundithawa koma inu Ambuye munachita kuthekera pano moyo wanga ndiwodalitsika mukhale nane Ambuye
Chorus
Ndayimba foni kumwamba Ambuye wandiyakha zokhumba mtima wanga zosowa pa moyo wanga Ambuye wandiyankha
Verse 2
Mukhale nane Ambuye munyengo ya mavuto munyengo ya mtendere ngakhale mu chilichonse muyende nane Ambuye ndinu odabwitsa mumachita chinthu chilichonse pakuti moyo wanga munawulenga kale munandidziwa ine.