MACFORD MWINI FILM MANDA ANABADWA PA 13 MARCH 1991 M’MUDZI WA MUJIMA BOMA LA MZIMBA. ANAYAMBA KUYIMBA CHAKA CHA 2011 NDI CHINYERA CYF ANATULUTSA ALBUM IMODZI YOCHEDWA MLANDU.
MU 2013 ANAPITA KU SOUTH AFRICA KOMWE ANAPANGA JOIN CHOIR YA SALVATION WORSHIPPERS NDIPO ANATULUTSA ALBUM IMODZI YOTCHEDWA MUNGAWANAZO NDALAMA.CHIFUKWA CHA VUTO LAZA CHUMA CHOIR INATHA MU CHAKA CHA 2020 NDIPAMENE ANAZIYIMIRA PA YEKHA. ALI NDI NYIMBO ZOKWANA 8 NDIPO SANATULUTSEPO ALBUM.