Choir ya Kempton Park CCAP
Salvation Choir inayamba pakale ndithu koma poyamba inali Tembisa praise team.
Koma chifukwa chakutsegulidwa kwa prayer house ina ma members ambiri a choir anapita ku prayer house ya new one yotchedwa Kempton Park CCAP prayer house.Apa mpomwe panadzabwera maganizo osintha dzina la Choir kukhala KEMPTON PARK SALVATION CHOIR ichi chinali Chaka cha 2015. Ndipo kuchokera pamenepo Choir yi yakwanitsa kutulutsa zimbale ziwiri zanyimbo zomvera(CD) komanso chimbale chimodzi chowonera (DVD). Chimbale choyamba anatulutsa mu chaka cha 2016 ndipo chachiwiri mu chaka cha 2018 Pamene DVD anatulutsa mu chaka cha 2021.