255
Kalambo CCAP Nursery Choir inayamba mu chaka cha 2006 ndipo imatumikira pa mpingo wa kalambo CCAP ku area 25 A mu mzinda wa Lilongwe. Yajambulapo zimbale zomvela zokwana zitatu ndi zowonela ziwiri ndipo ndi choir yomwe muli ana achichepele kwambiri.