Disciple Levison kamala
Album title Agwe
Nyimbo zonse wajambula Ku
MS studio (Cape Town)
Producer. Andy Chalamanda
Anabadwa pa 20/10 / 1980
Balaka, liwonde.Ndi okwatira ali ndi ana 4 all boys.Kumudzi Kwa bambo ndi Ku Zomba pomwe Kwa mayi ndi Ku Chiladzulu.
Anabadwira Ku Zomba komwe amakhala kwawo kwa bambo.
1994 anasamukila Ku liwonde,
1997 makolo ake onse anamwalira.
Ndi wa number 4 kubadwa kukhalaso last born mu banja lawo.
Anayamba kuyimba 2016
Iyi ndi album yake yoyamba.
Kupatula kuyimba amagwira ntchito (handyman) ku
South Africa (Cape Town) Since 2011.
Kuyimba ndi utumiki wake ndipo ndi chinthu chomwe amakonda kuchita pa moyo wake.