-
Blessed Nellie Mwale ndi M’busa wa Malawi Assemblies of God ndipo anabadwira ku Nkhotakota koma anakulira ku Lilongwe.Anabadwa pa 8/11/1987, m’banja mwawo anabadwa ana 5 ,Iyeyo ndi wa number 2 …
-
Ruth Misomali Serious Man anabadwira ku Chikwawa M’mudzi ndirande kukulira konko komanso ku Mulanje.Anabadwa pa 19 November 1991 ndipo m’banja mwawo anabadwa ana okwana 5 akazi atatu ndi amuna awili …
-
Saini Misoya anabadwa m’mudzi wa Sole, kuchididi boma la Nsanje.Saini Misoya anabadwa pa 14 February 1982,ndipo iyeyu anabadwa mubanja la ana khumi(10)ndipo ndimwana oyamba kubadwa. Saini Misoya anayamba kuimba ali …
-
Favour Chimpini Mkwamba anabadwa pa 5 /12/1995 ku Blantyre komaso kukulira Ku Blantyre komweko ndipo m’banja mwawo anabadwa ana okwana 8 koma omwe adatsala amoyo ndi 7 m’modzi adamwalira ndipo …
-
Mike Wiseman Tembo anabadwa pa 1 January 1989 Ku Chilimba Nkairo ndipo akulira kuchilimba komweko ndi Ku Nsanje pa Phokera T/A Mbenje chifukwa mayi ake anachita kulowoledwa koma pano amakhalira …
-
The Devil Challengers ndi gulu lomwe muli anyamata oyimba awiri ndipo anyamata amenewa mayina awo ndi Joel Majuni komaso Elijah Njirayagoma. Joel ndi ochokera m’mudzi mwa Rhoda mfumu yayikulu Kunthembwe/Chileka …
-
Patrick Makhumula was born in 1979 on 11 October and he is from Blantyre,Mdeka and his home village is Nthache village T/A Chugaru. He was born in a family of …
-
Born on 9th April 1982 at queens Elizabeth Hospital in Blantyre,Martin Lyton Came into Public eye with his hit song titled Tatulukako kuiguputo in 2017.Second born son in a family …
All Rights Reserved – Designed and Developed by Kay Dee Media