-
Mr Kazibweze Samuel Wilson anabadwira kwa T/A kuthembwe, kukulira komweko.Anabadwa pa 25 December 1989.M’banja mwawo anabadwa ana 8, ena anamwalira anatsala awiri ndipo iye ndi wa number 2. Wakumana ndi …
-
Precious anabadwira pachipatala cha Queen Elizabeth mu mzinda wa Blantyre,nthawi imeneyi mkuti makolo ake akukhala mdera lotchedwa chilimba.Precious ndi namba 3 pakubadwa ndipo m’banja mwawo alimo ana 6 amuna awiri, …
-
Davie Ronald Chirambo, 4th born son in a family of 6, Son of Brenda and Ronald Chirambo, from Msafire Village, T/A Mpherembe, Mzimba District. He is a soldier by professional …
-
𝖯𝖺𝗎𝗅 𝖫𝗅𝗈𝗒𝖽 𝖦𝖺𝗆𝖺 𝖺𝗇𝖺𝖻𝖺𝖽𝗐𝗂𝗋𝖺 𝗆’𝗆𝗎𝖽𝗓𝗂 𝗆𝗐𝖺 𝖬𝖺𝗄𝖺𝗍𝖺, 𝖳/𝖠 𝖢𝗁𝖺𝗆𝖻𝖺 𝖻𝗈𝗆𝖺 𝗅𝖺 M𝖺𝖼𝗁𝗂𝗇𝗀𝖺 ndipo w𝖺𝗄𝗎𝗅𝗂𝗋𝖺 𝗄𝗐𝖺 𝖳/𝖠 𝖫𝗂𝗐𝗈𝗇𝖽𝖾 𝗄𝗎 M𝖺𝖼𝗁𝗂𝗇𝗀𝖺 𝗄𝗈𝗆𝗐𝖾𝗄𝗈 𝗄𝗈𝗆𝖺 𝗉𝖺𝗇𝗈 𝖺𝗄𝗎𝗄𝗁𝖺𝗅𝖺 𝗄𝗐𝖺 𝖳/𝖠 𝖬𝗉𝗈𝗌𝖺, 𝖬𝖺𝖼𝗁𝗂n𝗀𝖺 ndipo a𝗇𝖺𝖻𝖺𝖽𝗐𝖺 𝗉𝖺 …
-
Luke Nyoni anabadwila komaso kukulira ku Mzimba T/A Mtwalo.Anabadwa pa 14 /12/1992 m’banja la ana 6 ndipo iye ndi wa number 4 m’modzi wanamba 3 anamwalira. Atabadwa dzina anamupatsa Luke …
-
SAMUEL SONGEYA NDI M’NYAMATA WOCHOKERA M,BOMA LA NTCHEU T/A INKOSI NJOLOMOLE,GV MUWALO CHAULUKA VILLAGE , GOWA MISSION SAM ANABADWA PA 01/09/1990 PA QUEEN ELIZABETH HOSPITAL (QUEENS )MU MZINDA WA BLANTYREPANTHAWI …
-
MJ Monty’s real name is Montfort Jenala who is coming from Chinyamula village T/A Kwataine in Ntcheu District.He was born on 12 April 1985 at Ntcheu District Hospital and born …
-
Lucy Chipembere anabadwa ndi kukulira m’boma la Kasungu koma kwawo kwa makolo ake ndi ku Dowa ndi Dedza kwa mai ndi bambo mu mndandanda otero.Ndipo iye anabadwa pa 15 July …
All Rights Reserved – Designed and Developed by Kay Dee Media