-
Genre: GospelCity: DedzaCountry: Malawi Matthew Kanyenda is a Malawian Gospel artist who comes from Mtakataka in Dedza district. He is also called Elisah Mneneri. He was born on 10 October, …
-
Mapulanga Francisco Vitsitsi, born on June 16, 1979, at St. Gabrielles Hospital in Lilongwe, Malawi. Hailing from a family of eight, with four brothers and four sisters, Mapulanga’s roots are …
-
Given Mulenga anabadwa pa 12 February 1992,School yake ya primary anaphunzira ku Chaba FP School P/O Box 86 Chitipa, Malawi kenaka anakapitiriza maphunziro ake ku Enukweni CDSS Mzimba. Kuchoka pamenepo …
-
Mphatso Haji Banda ndi oyimba nyimbo za Mulungu ndipo dzina la Banda ndi la amuna ake pomwe la Haji ndi la abambo ake. Iyeyu anabadwa mu chaka cha 1991 pa …
-
Ruth Chijani Zaipa anabadwa pa 24 May 1984 kwawo kochokela ndi ku Kasungu east kwa T,A Wimbe kwa Chamama. Ali pa banja ndi ana atatu. Chidwi chakuyimba adayamba ali wachichepele …
-
Samson Levi Chapo popularly known as Sam Chapo is a Mponela-based musician, producer, entrepreneur, and events manager. He was born on Octor 16 in the early 90s (exact year exhaled …
-
Yembekezani Kandadza anabadwa pa 3/3/1972 m’mudzi mwa Chiwaza T/A Chauma m’boma la Dedza. Anayamba kuyimba m’chaka cha 1995 pamene anayambitsa limodzi band,wayimbapo Chosen Warriors Band,Biriwita Mbenjere Band ndipo pano ali …
-
Rabson Mchizi anabadwa pa 18 December 1995, pa Ekwendeni hospital m’boma la Mzimba ndipo anabadwa mu nyumba ya ana 5 amuna 4 Mkazi m’modzi ndipo ndi mwana oyamba amene wakulila …
All Rights Reserved – Designed and Developed by Kay Dee Media